21.06.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

STRATEGIC IMPACT - SUKULU YOCHULUTSA AZITSOGOLELI

PHUNZILO 6 - UBYALA MIPINGO

“MFUNDO 2: PEMPHERO”

Pamene muyamba ukumana, gawanikani mʼmagulu ya anthu ANAI pagulu limodzi

pampindi zokwanila ngati makumi yatatu mwina mwache mochepekela.

Muphephererani wina ndi mzache ndipo mufunsane mafunso ya ungwilo. Pambuyo

pache nkhalaninso mʼmagulu anu ndiku werenga phunzilo ili ndiku ponyapo

ndemanga.

WERENGANI: Machitidwe 2:42, Akolose 4:2-4, Aroma12:12, 1 John 5:14-15, &

" " " Luka 10:2-3

! Mukayamba usintha maganizo yanu ku chokela ku maganizo yo manga Ufumu

wanu (zimango za ma chalichi/ma pologilamu/ndalama zambiri,ndi zina zache.) kuti

yakhali ma ganizo yo manga Ufumu wa Mulungu, muzaona zazikulu zomwe Mulungu

aku konzelani. Nchito yomwe Mulungu anati itanila ndiku pereka uthenga kwa anthu

wosowa” (Matteo 28:18-20, Machitidwe 1:8). Uphunzitsa amitundu ndi nchito ya

Mzimu Woyera (Yohane 6:65, 3:27). Utumiki wo pereka uthenga kwa anthu amitundu

ndi nchito ya mkristu aliyense ali padziko lapansi. kulibe munthu kapena gulu la anthu

omwe anga kwanise upereka uthenga ku mbali zonse za padziko lapansi pa iwo okha”

! Mulungu ati lamulila kuti ise tigwile nchito yo pambana pamvu zathu za umunthu.

Chakhala ngati chintu chapa fupi kwa ise kuti tiiwale nchito yo pereka ulaliki kwa

osowa. Yesu anati, “Ulamulilo wapadziko la kumwamba ndi dziko lapansi la patsidwa

kwa ine.” Analankhulanso kuti, “koma inu muzalandila mpamvu pamene Mzimu Oyera

adzadza pa inu.” Ngati mulungu atilamula, tikhulupirira kuti adza tipasa pamvu kenaka

zonse zofunikila kuti ifeyo tikwanilitse zomwe atilamulila – timupemphe Mulungu mwa

chi khulupiriro! Mu buku la 1Yohane 5:14-15, malemba yakuti, “And this is the

confidence that we have toward him, that if we ask anything according to his will he

hears us. And if we know that he hears us in whatever we ask, we know that we have

the requests that we have asked of him.” Ndikufunsani inuyo: kodi chikwanilitso cho

pereka uthenga kwa amitundu ndi chifunilo cha Mulungu? INDE ! INDE!! INDE!!!

Kodi Ambuye Yesu ali ndi mpamvu kuti akwanilitse nchito yo pereka ulaliki kwa

amitundu ? INDE! INDE!! INDE!!! Kodi chimenechi azachikwanilitsa bwanji?

Kupyolela mwa mpanvu Zache ndi zi nchito zathu!

NDEMANGA/MAFUNSO: Nichifukwa ninji timadalila mpamvu zathu, mpaso zathu kenaka

" ukatswili wathu kuti tikwanilise nchito yomwe Mulungu anatipasa?

! 30

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!