Create successful ePaper yourself
Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.
! Pamene muli ku penyetsetsa ndime muzapeza kuti muzakhala ndi mafunso

yakuti mudziwe tanthauzo yacha. Chachiwiri ndikufunsa mafunso yakulu yakulu

yomwe yazathandiza kuti LONGOSOLANI kapena kuti mvetsetse malemba (mabuku

ya konkodansi ndi mabuku yo masulila tanthauzo yamau kapena kuti dikishonali

niyofunikila kwambiri)

NDEMANGA/MAFUNSO: Pazomwe mwapeza mu buku ya 2 Timoteo 1:7, yankhani funso

" iyi ya dongosolo: “ndi zotani zomwe zinali uchitika pakati ka anthu anali utengako

" mbali panthawi imeneyi?”

UMASULILA

Ndi mau yoti yomwe tifunika kumasulila? Ndi zithu zotani za kale kapena za maloyo Ndi zotani zomwe zinali uchitika pakati ka

kapenanso za myiambo zomwe zinali anthu anali utengako mbali panthawi

kuchitika panthawi imeneyi?

imeneyi?

How is something to be done or

accomplished?

Mwamphunzilapo chiani pakhalidwe ya

anthu kapena khalidwe yanu?

Kodi nichifukwa ninji izi zina lankhulidwe Kodi muphunzilapo ciani pa za Mulungu,

Yesu, ndi Muzimu Oyela?

Tayankhani mafunso yayakulu kuti

mumvetsetsetse ndime yomwe

mukuwerenga?

Talembani mwachi ndunji choonadi

chimodzi chomwe mwachiona mundime

yomwe mwawerenga:

! 36