21.06.2013 Views

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

Tsiku 1 - strategic impact

SHOW MORE
SHOW LESS

Create successful ePaper yourself

Turn your PDF publications into a flip-book with our unique Google optimized e-Paper software.

STRATEGIC IMPACT - SUKULU YOCHULUTSA AZITSOGOLELI

MPHUNZILO 7 - UTUKULA ZA UMOYO

“MOWERENGELA MAU AMULUNGU”

Pamene muyamba ukumana, gawanikani mʼmagulu ya anthu ANAI pagulu limodzi

pampindi zokwanila ngati makumi yatatu mwina mwache mochepekela.

Muphephererani wina ndi mzache ndipo mufunsane mafunso ya ungwilo. Pambuyo

pache nkhalaninso mʼmagulu anu ndiku werenga phunzilo ili ndiku ponyapo

ndemanga.

! Mulungu anatipasa mau ache kuti timphindulile kuzinshito zonse zabwino (2

Timoteo 3:16-17). Tifunikila kuwerenga ndi kusewenzesa mau amulungu mozipereka

ndiku phunzisa anthu amene tikutumikila.

Kuli makwelelo yatatu yayakulu yafunikila powerenga mau Amulungu:

1. Penyetsetsani - Malemba yaku lankhula chiani?

2. Masulilani - Malemba yatanthauza chiani?

3. Masewenzeso - ndizotani zimene tifunikila uchita kapena usintha kulingana ndi

mau yomwe yawerengendwa?

NDEMANGA/MAFUNSO: nichifukwa ninji chimene tifunikila kuchita zinthu zitatuzi kuti

" timvetsetsetse mau A mulungu?

Tifunika zida zambiri zotithandizila powerenga mau Amulungu:

1) Baibulo.

2) Nthawi - sankhani nthawi sabata iliyonse kuti muwerenge mau Amulungu.

3) Phensulu ndi pepala - lembani zomwe mukuphunzila powerenga mau.

4) Buku yothandizila upeza malemba kapena konkodansi.

5) Buku yomasulile tanthauzo ya mau ya Baibulo.

NDEMANGA/MAFUNSO: Pa izi zachulidwa ndiziti zomwe mukufunitsitsa ndipo

" mungazipeze motani?

! Makwelelo yoyamba powerenga Baibulo NDIKUPENYETSETSA MBALI

YAMALEMBA. Sankhani ndime, kapena malemba yomwe muzawerenga ndiku

yankha mafunso yosatila. (Tengani nthawi yokwanila powerenga mau):

! 34

Hooray! Your file is uploaded and ready to be published.

Saved successfully!

Ooh no, something went wrong!