You also want an ePaper? Increase the reach of your titles
YUMPU automatically turns print PDFs into web optimized ePapers that Google loves.
STRATEGIC IMPACT - SUKULU YOCHULUTSA AZITSOGOLELI

PHUNZILO 10 - UTUKULA ZA UMOYO

“CHITSANZO CHAPEPHERO - PEMPERO YA AMBUYE”

Pamene muyamba ukumana, gawanikani mʼmagulu ya anthu ANAI pagulu limodzi

pampindi zokwanila ngati makumi yatatu mwina mwache mochepekela.

Muphephererani wina ndi mzache ndipo mufunsane mafunso ya ungwilo. Pambuyo

pache nkhalaninso mʼmagulu anu ndiku werenga phunzilo ili ndiku ponyapo

ndemanga.

WELENGANI: Mateyo 6:5-15

! Pemphero ndiye njila yakuyanjanitsa inu ndi Mulungu. Ngati akristo, Mulungu

anati pasa ndanga kuti tidze kwa iye, Mlengi wa zonse ndiponso Mfumu wa zonse.

Pakuti malemba yati sonyeza malamulo momwe tinga pempherere, ndiye kuti kulinso

njila yo vomekezedwa ndi yo savomekezedwa po bwera pamaso pa Mulungu. Ambuye

yesu anati phunzitsa momwe tiyenela kupepherera. Mu buku la Mateo 6:5-8 Ambuye

Yesu anatipasa malamulu yomwe tiyenela kusata tisane pemphere, mu Mateo 6:9-13.

Ambuyeanatipasa pemphero mwachitsanzo. Mu Mateo 6:14-15 anati pansanso ku

unikilidwa kut pemphero ifunikila ku khali ndi choonadi.

ZOFUNIKILA TISANAYAMBE UPEMPHELA:

Mateo 6:5-6 Ilankhula kuti tisama phemphera ngati “achinyengo”. Simupemphera

kuti muonekele ku anthu. Simupephera kuti mukodweretse anthu ndi mau apemphero

lanu. Anthu ambili agwa mu msapha umeneyu kuti akaonekele ali kupemphera pagulu

la anthu kuti anthu atione ngati auzimu kapena akatswili amapephero. Mwa choonadi

mtima wathu ukufube ulemelelo wathu osati wa Mulungu. Chimenechi chitsonyeza kuti

ise sindise Auzimua!

! Popephera ndicho funikila kuti mulowe mchipinda muli mwekha. Mulungu ama

timva ngakhale pomwe tili mʼmalo achisinsi. Kodi chimenechi chitanthauza kuti sitinga

pemphere pa gulu ya anthu? Kodi chilibwanji chimenechi? Pemphero ya chitsanzo pa

ndime 7-13 ina perekedwa pakati pa iwo omwe Ambuye Yesu anali kuphunzitsa. Kuli

zitsanzo zambili mchipangano chatsopano pomwe mapemphero yana perekedwa pa

gulu la anthu. Sikuchimwa ai ngati tiku pemphera pa gulu la anthu, koma ndi chimo

ngati tiku pemphera ngati achinyengo- kuti tionekele ku anthu. Ngati simukwanilisa

upemphera pagulu popanda kugwa mumuyeso uwu ndi bwino kupita kwa mwekha

kuka pemphera.

NDEMANGA/MAFUNSO: Kodi tinga pewe bwanji chikhalidwe chopemphera kuti tionekele

" ku anthu?

! 44